Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 Dulani makadiwa kuti akuthandizeni kuloweza mabuku ena a m’Baibulo a Malemba a Chiheberi. Funsani anthu a m’banja mwanu komanso anzanu. Genesis Buku lofotokoza mmene paradaiso anathera Ekisodo Mulungu anapulumutsa anthu ake modabwitsa Levitiko Malamulo a Mulungu anawathandiza kukhala oyera tsiku lililonse Numeri Ena analephera kukalowa m’Dziko Lolonjezedwa KHALANI BWENZI LA YEHOVA ZOCHITA s PINDANI PINDANI www.jw.org 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Tsamba 1
6
Embed
Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA
This document is posted to help you gain knowledge. Please leave a comment to let me know what you think about it! Share it to your friends and learn new things together.
Transcript
Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1Dulani makadiwa kuti akuthandizeni kuloweza mabuku ena a m’Baibulo a Malemba aChiheberi. Funsani anthu a m’banja mwanu komanso anzanu.
GenesisBuku lofotokoza
mmene paradaiso anathera
EkisodoMulungu anapulumutsaanthu ake modabwitsa
LevitikoMalamulo a Mulungu
anawathandiza kukhalaoyera tsiku lililonse
NumeriEna analephera kukalowa
m’Dziko Lolonjezedwa
KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA
s
PINDANI
PINDANI
www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 1